Best Malawi Online Juga

Nawu mndandanda wa bwino Malawi Intaneti juga! Pitirirani ndipo onani tsamba athu ndi kupeza onse pamwamba Malawi Intaneti juga!
Show more Hide

Mobile friendly

Players are welcome

None

Filter

Sort by:

None

Sort by:

Promoted
Latest
Best Casinos
Bonus Rating
Trust Rating
Game Rating
Usability Rating

3.2

 • 4.4
 • 3.9
 • 2.1
 • 2.5
Bonus 100% I 100 SPINÓW W STARBURST!
 • Launched 30.Nov.2019
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, Pragmatic Play, Betsoft
 • Licenсes Curaçao

Bonus fornew customers,

WR40x,

Min Dep €20

3

 • 2.5
 • 3.8
 • 2
 • 3.8
100% up to €500 + 100 Free Spins
 • Launched 08.Mar.2020
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, Pragmatic Play, Betsoft
 • Licenсes Curaçao

WR30x,

Min Dep €20

2.6

 • 4.4
 • 1.6
 • 2.5
 • 1.8
200% Welcome Bonus + 25 Free Spins
 • Launched 07.Jun.2016
 • Software Rival
 • Licenсes Curaçao

WR40x,

Min Dep $25,

CodeLOVELY200

2.7

 • 2.5
 • 2.5
 • 2.5
 • 3.5
100% Bonus Up To €200 On Your First Deposit
 • Launched 2016
 • Software NetEnt, Microgaming, Pragmatic Play, Betsoft, Play'n GO
 • Licenсes Curaçao

WR30x,

Min Dep €10

3

 • 2.5
 • 3.7
 • 2.1
 • 3.8
100% Bonus up to €500 + 200 Free Spins
 • Launched 2019
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, NextGen, Pragmatic Play
 • Licenсes Curaçao

WR30x,

Min Dep €20

3.2

 • 2.5
 • 4.2
 • 2.2
 • 3.8
100% Bonus up to €500 and 200 Free Spins
 • Launched 31.Dec.2018
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, Pragmatic Play, Betsoft
 • Licenсes Curaçao

WR30x,

Min Dep €20

Kodi muli ku Malawi ndipo mukufuna kupha makwacha? Ngati ndi choncho, kasino ingakuthandizeni. Koma mwina simukufuna kuyenda ndi kupita kumalo komwe kuli kasino. Kodi mukudziwa kuti tsopano mukhoza kupeza malo ngati amene pa intaneti? Chofunika ndi foni kapena kompyuta ndiponso intaneti basi. Ndipotu makasino a pa intaneti ndi ovomerezeka ndi malamulo a boma.

Iphani Makwacha pa Kasino ya pa Intaneti m’Malawi!

Njira za msangulutso ndi zambiri ndipo pochita msangulutsowu mungaphenso makwacha. Kodi mukudziwa kuti mukhoza kupita ku kasino n’kukasanguluka kwinaku mukuphanso makwacha? Kumeneku ndiko kupha mbalame ziwiri ndi mwala umodzi. Nanga bwanji kusewera pa foni yanu kapena kompyuta? Tadikirani kaye ndikufotokozerani. Ngakhale kuti dziko la Malawi lino ndi losauka ndipo anthu ena amaganiza kuti sizingatheke kukhala mponda matiki ndipo amasankha kupita ku mayiko ena kukasaka chuma, n’zotheka kupeza ndalama zambiri popanda kukhetsera thukuta komanso m’njira yovomerezeka ndi boma.

Kodi Malamulo a Dziko la Malawi Amavomereza?

Inde! M’chaka cha 1996, boma la Malawi linapanga malamulo ovomereza njira zina zopezera ndalama posewera magemu osiyanasiyana pa intaneti, posewera magemu ena a pa kompyuta kapena pa foni, ngakhalenso pobetcha kudzera ku makampani ovomerezaka obetcherana. Njira zimenezi n’zosiyana kwambiri ndi juga chifukwa munthu amachita msangulutso kwinaku akupha makwacha m’njira yovomerezeka ndi malamulo a dziko lino la Malawi. Komatu makampani omwe ali ndi makasino ndiponso omwe ayendetsa zokhudza kubetcherana alipo ambirimbiri.

Pakafukufuku wina amene anachitika mu 2015, zinadziwika kuti mwa anthu opitirira 17 miliyoni amene ali m’Malawi muno, anthu opitirira 6.3 miliyoni ali ndi mafoni a m’manja poyerekezera ndi anthu 45,700 omwe amadalira kwambiri mafoni a m’nyumba kapena muofesi okhala ndi nthambo. Zimenezi zikusonyeza kuti anthu omwe amagwiritsa ntchito mafoni a m’manjawa angathe kupha makwacha ngati atasankha kuchita masewera obetcherana.

Kodi Kasino Yabwino Mungaidziwe Bwanji?

Pali zinthu zambiri zimene zingakuthandize kuti mudziwe ngati kasino ili yabwino kwambiri kapena ayi. Taonani zina mwa zotsatirazi:

- Iyenera kukhale ndi gemu ya makadi: Imeneyi ndi gemu yomwe munthu amasewera pa kompyuta kapena pa makina ena, ndipo pali mitundu yambiri ya gemu imeneyi. Munthu angasewere yekha kapena anthu angapo angakonze timagulu kapena matimu n’kusewera mopikisana. Chofunika n’kuika kandalama kochepa m’makina kuti makinawo kapena kompyuta iyambe kusonyeza makadi amene mungasewere. Anthu a mphumi pa gemuyi amatha kuwina ndalama za nkhaninkhani m’kanthawi kochepa kwambiri.

- Ikhale ndi gemu ya manambala: Gemu imeneyi ingaseweredwenso ndi munthu mmodzi kapena angapo pa nthawi imodzi. Chofunika n’kungoika ndalama pa nambala imene munthu wasankha, yomwe uli pa bodi yozungulira yokhala ndi manambala ambirimbiri. Bodiyo akazungulira kenako n’kuima oyang’anizana ndi pa malo pamene pali nambala yomwe munthu waikapo ndalama ndiye kuti munthuyo wapambana. Zonsezi zimachitika pa makina a jakipoti kapena pa kompyuta.

- Ikhale ndi ziphaso zovomerezeka ndi boma: Kasino iliyonse yovomerezeka imayenera kulembedwa ku boma mogwirizana ndi malamulo a dziko la Malawi. Ubwino wochita zimenezi ndi wakuti anthu omwe akufika kudzachita msangulutso ndi kupha makwacha amakhala otetezeka ndipo sangaberedwe ndalama zawo ndi makina achinyengo. Komanso ngati patachitika ngozi yadzidzidzi yomwe yakhudza anthu omwe ali mu kasino yotereyi, ovulalawo amayenera kulandira chipepeso kuchokera kwa eni a malowo, mogwirizana ndi malamulo.

- Kupereka ndalama kwa anthu omwe apambana: Imayenera kupereka ndalama pompopompo kwa anthu onse amene apambana pa jakipoti.

- Mapulogalamu a pakompyuta: Mapulogalamu a pakompyuta osewerera magemu a mu kasino amayenera kukhala osavuta kuwagwiritsa ntchito kuti aliyense akwanitse kuchita nawo msangulutso wa jakipoti.

Mawu Omaliza

Malinga ndi zimene taonazi, n’zotheka ndithu munthu kukhala mponda matiki ku Malawi komwekuno popanda kupita kukagwira ntchito m’mayiko akunja. Ndipo zimenezi zingatheke popanda kukhetsa thukuta ngakhale pang’ono! Nkhani yake ndi jakipoti basi! Inde, onetsetsani kuti kasino imene mukupitako ndi yovomerezeka ndi boma.